Luka 2:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Mu ola limenelo iye anafika pafupi nʼkuyamba kuyamika Mulungu komanso kulankhula zokhudza mwanayo kwa onse amene ankayembekezera chipulumutso cha Yerusalemu.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:38 Nsanja ya Olonda,5/15/1994, tsa. 2710/15/1990, tsa. 14 1. Kuwala Kwenikweni kwa Dziko Malifalensi a Mavidiyo a Uthenga Wabwino wa Yesu Anna analankhula zokhudza mwanayo (gnj 1 48:52–50:21)
38 Mu ola limenelo iye anafika pafupi nʼkuyamba kuyamika Mulungu komanso kulankhula zokhudza mwanayo kwa onse amene ankayembekezera chipulumutso cha Yerusalemu.+