-
Luka 2:43Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
43 Chikondwererocho chitatha, iwo ananyamuka kubwerera kwawo. Koma mnyamatayo Yesu anatsalira ku Yerusalemu ndipo makolo ake sanadziwe zimenezo.
-
-
1. Kuwala Kwenikweni kwa DzikoMalifalensi a Mavidiyo a Uthenga Wabwino wa Yesu
-
-
Zimene Yesu anachita kukachisi ali ndi zaka 12 (gnj 1 1:04:00–1:09:40)
-