-
Luka 2:44Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
44 Iwo ankaganiza kuti iye anali nawo mʼgulu la anthu a pa ulendowo, moti anayenda ulendo wa tsiku lathunthu. Kenako anayamba kumufunafuna mwa achibale ndi anzawo.
-
-
1. Kuwala Kwenikweni kwa DzikoMalifalensi a Mavidiyo a Uthenga Wabwino wa Yesu
-
-
Zimene Yesu anachita kukachisi ali ndi zaka 12 (gnj 1 1:04:00–1:09:40)
-