-
Luka 2:46Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
46 Ndiyeno patatha masiku atatu, anamupeza ali mʼkachisi, atakhala pakati pa aphunzitsi ndipo ankawamvetsera nʼkumawafunsa mafunso.
-
-
1. Kuwala Kwenikweni kwa DzikoMalifalensi a Mavidiyo a Uthenga Wabwino wa Yesu
-
-
Zimene Yesu anachita kukachisi ali ndi zaka 12 (gnj 1 1:04:00–1:09:40)
-