-
Luka 2:48Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
48 Makolo akewo atamuona anadabwa kwambiri, ndipo mayi ake anamufunsa kuti: “Mwanawe, nʼchifukwa chiyani wativutitsa chonchi? Ine ndi bambo akowa tinali ndi nkhawa kwambiri ndipo timakufunafuna.”
-
-
1. Kuwala Kwenikweni kwa DzikoMalifalensi a Mavidiyo a Uthenga Wabwino wa Yesu
-
-
Zimene Yesu anachita kukachisi ali ndi zaka 12 (gnj 1 1:04:00–1:09:40)
-