Luka 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ankachita zimenezi mogwirizana ndi zimene zinalembedwa mʼbuku la mawu a Mneneri Yesaya kuti: “Winawake akufuula mʼchipululu kuti: ‘Konzani njira ya Yehova!* Muwongole misewu yake.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:4 Yesaya 1, ptsa. 399-401
4 Ankachita zimenezi mogwirizana ndi zimene zinalembedwa mʼbuku la mawu a Mneneri Yesaya kuti: “Winawake akufuula mʼchipululu kuti: ‘Konzani njira ya Yehova!* Muwongole misewu yake.+