-
Luka 3:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Chigwa chilichonse chikwiriridwe, ndipo phiri lililonse ndi chitunda chilichonse zisalazidwe. Njira zokhotakhota zikhale zowongoka ndipo malo okumbikakumbika akhale osalaza bwino.
-