Luka 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iye anawayankha kuti: “Munthu amene ali ndi zovala ziwiri agawireko munthu amene alibiretu ndipo amene ali ndi chakudya achitenso chimodzimodzi.”+
11 Iye anawayankha kuti: “Munthu amene ali ndi zovala ziwiri agawireko munthu amene alibiretu ndipo amene ali ndi chakudya achitenso chimodzimodzi.”+