Luka 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Asilikali nawonso ankamufunsa kuti: “Kodi tichite chiyani?” Ndipo iye ankawauza kuti: “Musamavutitse anthu* kapena kuimba aliyense mlandu wabodza,+ koma muzikhutira ndi zimene mumalandira.”*
14 Asilikali nawonso ankamufunsa kuti: “Kodi tichite chiyani?” Ndipo iye ankawauza kuti: “Musamavutitse anthu* kapena kuimba aliyense mlandu wabodza,+ koma muzikhutira ndi zimene mumalandira.”*