Luka 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako Yesu anachoka ku Yorodano atadzazidwa ndi mzimu woyera ndipo mzimuwo unamutenga nʼkumuyendetsa malo osiyanasiyana mʼchipululu+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:1 Nsanja ya Olonda,12/15/2011, tsa. 15
4 Kenako Yesu anachoka ku Yorodano atadzazidwa ndi mzimu woyera ndipo mzimuwo unamutenga nʼkumuyendetsa malo osiyanasiyana mʼchipululu+