Luka 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Poyankha Yesu anamuuza kuti: “Malemba amati, ‘Yehova* Mulungu wanu musamamuyese.’”+