-
Luka 4:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Atatero anapinda mpukutuwo nʼkuubwezera kwa wotumikira mmenemo ndipo anakhala pansi. Maso a anthu onse amene anali mʼsunagogemo anali pa iye nʼkumamuyangʼanitsitsa.
-