Luka 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Zitatero onse anayamba kumutamanda komanso anadabwa ndi mawu ogwira mtima amene anatuluka pakamwa pake,+ moti ankanena kuti: “Kodi si mwana wa Yosefe ameneyu?”+
22 Zitatero onse anayamba kumutamanda komanso anadabwa ndi mawu ogwira mtima amene anatuluka pakamwa pake,+ moti ankanena kuti: “Kodi si mwana wa Yosefe ameneyu?”+