Luka 4:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atamva zimenezi iye anawauza kuti: “Mosakayikira mudzagwiritsa ntchito pa ine mawu akuti, ‘Wochiritsa iwe, dzichiritse wekha. Zinthu zambiri zimene tinamva kuti unachita ku Kaperenao,+ uzichitenso kwanu kuno.’” Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:23 Yesu—Ndi Njira, tsa. 56 Nsanja ya Olonda,2/15/1986, tsa. 8
23 Atamva zimenezi iye anawauza kuti: “Mosakayikira mudzagwiritsa ntchito pa ine mawu akuti, ‘Wochiritsa iwe, dzichiritse wekha. Zinthu zambiri zimene tinamva kuti unachita ku Kaperenao,+ uzichitenso kwanu kuno.’”