Luka 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mwachitsanzo, ndithu ndikukuuzani kuti: Munali akazi ambiri amasiye mu Isiraeli mʼmasiku a Eliya, pamene kumwamba kunatsekedwa kwa zaka zitatu ndi miyezi 6 ndipo mʼdziko lonse munali njala yaikulu.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:25 Nsanja ya Olonda,4/1/2008, tsa. 194/1/1992, tsa. 17
25 Mwachitsanzo, ndithu ndikukuuzani kuti: Munali akazi ambiri amasiye mu Isiraeli mʼmasiku a Eliya, pamene kumwamba kunatsekedwa kwa zaka zitatu ndi miyezi 6 ndipo mʼdziko lonse munali njala yaikulu.+