Luka 4:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndiponso munali akhate ambiri mu Isiraeli mʼnthawi ya mneneri Elisa. Komabe palibe aliyense wa iwo amene anayeretsedwa,* koma Namani wa ku Siriya.”+
27 Ndiponso munali akhate ambiri mu Isiraeli mʼnthawi ya mneneri Elisa. Komabe palibe aliyense wa iwo amene anayeretsedwa,* koma Namani wa ku Siriya.”+