-
Luka 4:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Iwo ananyamuka ndipo mwamsangamsanga anamutulutsira kunja kwa mzinda. Kenako anapita naye pamwamba pa phiri pamene panali mzinda wawo, kuti akamuponye kuphedi.
-