Luka 4:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kumeneko anthu anadabwa kwambiri ndi kaphunzitsidwe kake,+ chifukwa ankalankhula mosonyeza kuti ali ndi ulamuliro.
32 Kumeneko anthu anadabwa kwambiri ndi kaphunzitsidwe kake,+ chifukwa ankalankhula mosonyeza kuti ali ndi ulamuliro.