-
Luka 4:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Ataona zimenezi anthu onse anadabwa kwambiri ndipo anayamba kukambirana kuti: “Taonani, mawu ake ndi amphamvu kwambiri! Chifukwa akutha kudzudzula mizimu yonyansa mwa ulamuliro ndi mphamvu ndipo mizimuyo ikutulukadi.”
-