Luka 4:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Atatuluka mʼsunagogemo, anakalowa mʼnyumba ya Simoni. Pa nthawiyo apongozi aakazi a Simoni ankadwala malungo aakulu,* choncho anamupempha kuti awathandize.+
38 Atatuluka mʼsunagogemo, anakalowa mʼnyumba ya Simoni. Pa nthawiyo apongozi aakazi a Simoni ankadwala malungo aakulu,* choncho anamupempha kuti awathandize.+