-
Luka 4:39Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
39 Ndiyeno anaima pamene mayiwo anagona nʼkuwachiritsa ndipo malungowo anatheratu. Nthawi yomweyo mayiwo anadzuka nʼkuyamba kuwatumikira.
-