Luka 4:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Koma pamene dzuwa linkalowa, onse amene anali ndi anthu odwala matenda osiyanasiyana anawabweretsa kwa iye. Ndipo iye anawachiritsa poika manja ake pa iwo.+
40 Koma pamene dzuwa linkalowa, onse amene anali ndi anthu odwala matenda osiyanasiyana anawabweretsa kwa iye. Ndipo iye anawachiritsa poika manja ake pa iwo.+