Luka 4:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ziwanda nazonso zinatuluka mwa anthu ambiri zikufuula kuti: “Inu ndinu Mwana wa Mulungu.”+ Koma iye anadzudzula ziwandazo ndipo sanazilole kuti zilankhule+ chifukwa zinkamudziwa kuti ndi Khristu.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:41 Yesu—Ndi Njira, tsa. 60
41 Ziwanda nazonso zinatuluka mwa anthu ambiri zikufuula kuti: “Inu ndinu Mwana wa Mulungu.”+ Koma iye anadzudzula ziwandazo ndipo sanazilole kuti zilankhule+ chifukwa zinkamudziwa kuti ndi Khristu.+