Luka 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno iye anaona ngalawa ziwiri ataziimika mʼmphepete mwa nyanjayo, koma asodzi anali atatsikamo ndipo ankachapa maukonde awo.+
2 Ndiyeno iye anaona ngalawa ziwiri ataziimika mʼmphepete mwa nyanjayo, koma asodzi anali atatsikamo ndipo ankachapa maukonde awo.+