-
Luka 5:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Choncho iye analowa mʼngalawa imodzi, imene inali ya Simoni ndipo anamupempha kuti aisunthire mʼmadzi pangʼono. Kenako anakhala pansi mʼngalawamo nʼkuyamba kuphunzitsa gulu la anthulo.
-