-
Luka 5:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ataona zimenezi, Simoni Petulo anagwada pamaso pa Yesu ndipo anamuuza kuti: “Ambuye, chokani pali ine pano chifukwa ndine munthu wochimwa.”
-