Luka 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako panafika anthu atanyamula munthu wakufa ziwalo pamachira. Iwo ankafunafuna njira yoti amulowetsere mʼnyumbamo nʼkukamuika pafupi ndi Yesu.+
18 Kenako panafika anthu atanyamula munthu wakufa ziwalo pamachira. Iwo ankafunafuna njira yoti amulowetsere mʼnyumbamo nʼkukamuika pafupi ndi Yesu.+