Luka 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako alembi ndi Afarisi anayamba kudzifunsa kuti: “Kodi ameneyu ndi ndani kuti azinyoza Mulungu chonchi? Winanso ndi ndani amene angakhululukire machimo kupatulapo Mulungu?”+
21 Kenako alembi ndi Afarisi anayamba kudzifunsa kuti: “Kodi ameneyu ndi ndani kuti azinyoza Mulungu chonchi? Winanso ndi ndani amene angakhululukire machimo kupatulapo Mulungu?”+