Luka 5:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma kuti mudziwe kuti Mwana wa munthu ali ndi mphamvu padziko lapansi zokhululukira machimo—” kenako anauza wakufa ziwalo uja kuti: “Ndikunena ndi iwe, Nyamuka, tenga machira akowa ndipo uzipita kwanu.”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:24 Yesu—Ndi Njira, tsa. 67 Nsanja ya Olonda,5/1/1986, tsa. 9
24 Koma kuti mudziwe kuti Mwana wa munthu ali ndi mphamvu padziko lapansi zokhululukira machimo—” kenako anauza wakufa ziwalo uja kuti: “Ndikunena ndi iwe, Nyamuka, tenga machira akowa ndipo uzipita kwanu.”+