Luka 5:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kenako Levi anakonzera Yesu phwando lalikulu kunyumba kwake. Kumeneko kunabwera anthu ambiri okhometsa msonkho komanso ochimwa ndipo ankadya* limodzi ndi Yesu komanso ophunzira ake.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:29 Yesu—Ndi Njira, tsa. 68 Nsanja ya Olonda,5/15/1986, ptsa. 8-9
29 Kenako Levi anakonzera Yesu phwando lalikulu kunyumba kwake. Kumeneko kunabwera anthu ambiri okhometsa msonkho komanso ochimwa ndipo ankadya* limodzi ndi Yesu komanso ophunzira ake.+