Luka 5:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Iwo anamuuza kuti: “Ophunzira a Yohane amasala kudya kawirikawiri ndipo amapemphera mopembedzera. Ophunzira a Afarisi amachitanso chimodzimodzi, koma anuwa amangodya ndi kumwa.”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:33 Yesu—Ndi Njira, tsa. 70 Nsanja ya Olonda,6/1/1986, ptsa. 8-9
33 Iwo anamuuza kuti: “Ophunzira a Yohane amasala kudya kawirikawiri ndipo amapemphera mopembedzera. Ophunzira a Afarisi amachitanso chimodzimodzi, koma anuwa amangodya ndi kumwa.”+