Luka 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsiku lina pa tsiku la sabata, Yesu ankadutsa mʼmunda wa tirigu ndipo ophunzira ake ankabudula ngala za tirigu+ nʼkumazitikita mʼmanja mwawo kenako nʼkudya.+
6 Tsiku lina pa tsiku la sabata, Yesu ankadutsa mʼmunda wa tirigu ndipo ophunzira ake ankabudula ngala za tirigu+ nʼkumazitikita mʼmanja mwawo kenako nʼkudya.+