-
Luka 6:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Alembi ndi Afarisi ankamuyangʼanitsitsa kuti aone ngati angachiritse munthuyo pa Sabata nʼcholinga choti amuimbe mlandu.
-