Luka 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma iye anadziwa zimene iwo ankaganiza.+ Choncho anauza munthu wolumala dzanjayo kuti: “Nyamuka, bwera pakatipa.” Munthuyo ananyamuka nʼkuima pamenepo.
8 Koma iye anadziwa zimene iwo ankaganiza.+ Choncho anauza munthu wolumala dzanjayo kuti: “Nyamuka, bwera pakatipa.” Munthuyo ananyamuka nʼkuima pamenepo.