-
Luka 6:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Kenako anatsika nawo nʼkukaima pamalo afulati. Pamenepo panali gulu lalikulu la ophunzira ake. Panalinso chigulu cha anthu ochokera ku Yudeya konse ndi ku Yerusalemu konse, komanso kumadera amʼmphepete mwa nyanja a ku Turo ndi ku Sidoni. Onsewo anabwera kuti adzamumvetsere komanso kuti adzawachiritse.
-