Luka 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Gulu lonse la anthulo linkayesetsa kuti limugwire, chifukwa mphamvu zinkatuluka mwa iye+ nʼkuchiritsa anthu onsewo. Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:19 Nsanja ya Olonda,2/15/1987, tsa. 9
19 Gulu lonse la anthulo linkayesetsa kuti limugwire, chifukwa mphamvu zinkatuluka mwa iye+ nʼkuchiritsa anthu onsewo.