Luka 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndinu osangalala anthu akamadana nanu,+ kukusalani,+ kukunyozani komanso kukana* dzina lanu nʼkumanena kuti ndi loipa, chifukwa cha Mwana wa munthu. Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:22 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),7/2019, ptsa. 6-7 Nsanja ya Olonda,10/1/1990, tsa. 23
22 Ndinu osangalala anthu akamadana nanu,+ kukusalani,+ kukunyozani komanso kukana* dzina lanu nʼkumanena kuti ndi loipa, chifukwa cha Mwana wa munthu.