Luka 6:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Tsoka inu amene mukukhuta panopa, chifukwa mudzamva njala. Tsoka inu amene mukuseka panopa, chifukwa mudzamva chisoni komanso kulira.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:25 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 85-86 Nsanja ya Olonda,3/15/1987, tsa. 11
25 Tsoka inu amene mukukhuta panopa, chifukwa mudzamva njala. Tsoka inu amene mukuseka panopa, chifukwa mudzamva chisoni komanso kulira.+