Luka 6:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Muli ndi tsoka anthu onse akamanena zabwino za inu,+ popeza zinthu zimenezo ndi zimenenso makolo awo akale anachitira aneneri abodza. Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:26 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 85-86 Nsanja ya Olonda,3/15/1987, tsa. 11
26 Muli ndi tsoka anthu onse akamanena zabwino za inu,+ popeza zinthu zimenezo ndi zimenenso makolo awo akale anachitira aneneri abodza.