Luka 6:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Amene wakumenya mbama patsaya ili, umupatsenso linalo. Amene wakulanda malaya ako akunja, usamuletse kutenga malaya ako amkati.+
29 Amene wakumenya mbama patsaya ili, umupatsenso linalo. Amene wakulanda malaya ako akunja, usamuletse kutenga malaya ako amkati.+