Luka 6:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Aliyense amene wakupempha kanthu mupatse,+ ndipo amene wakulanda zinthu usamuumirize kuti abweze.