Luka 6:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Pitirizani kukhala achifundo, mofanana ndi Atate wanu amenenso ndi wachifundo.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:36 Nsanja ya Olonda,4/15/1987, tsa. 27