Luka 6:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Mtengo wabwino sungabereke chipatso chowola ndipo mtengo wowola sungabereke chipatso chabwino.+