Luka 6:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Munthu wabwino amatulutsa zabwino mʼchuma chabwino chamumtima mwake, koma munthu woipa amatulutsa zoipa mʼchuma choipa chamumtima mwake, chifukwa pakamwa pamalankhula zosefukira mumtima.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:45 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 51 Nsanja ya Olonda,10/15/2001, ptsa. 23-24
45 Munthu wabwino amatulutsa zabwino mʼchuma chabwino chamumtima mwake, koma munthu woipa amatulutsa zoipa mʼchuma choipa chamumtima mwake, chifukwa pakamwa pamalankhula zosefukira mumtima.+