Luka 6:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Aliyense amene amabwera kwa ine kudzamva mawu anga, nʼkuchita zimene wamvazo, ndikuuzani amene amafanana naye:+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:47 Nsanja ya Olonda,1/1/2007, tsa. 32
47 Aliyense amene amabwera kwa ine kudzamva mawu anga, nʼkuchita zimene wamvazo, ndikuuzani amene amafanana naye:+