Luka 6:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Iyeyo ali ngati munthu amene pomanga nyumba, anakumba mozama kwambiri nʼkuyala maziko pathanthwe. Ndiye mtsinje utasefukira, madzi anawomba nyumbayo, koma sanathe kuigwedeza chifukwa anaimanga bwino.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:48 Nsanja ya Olonda,11/1/2008, ptsa. 29-311/1/2007, tsa. 3210/1/1990, tsa. 24
48 Iyeyo ali ngati munthu amene pomanga nyumba, anakumba mozama kwambiri nʼkuyala maziko pathanthwe. Ndiye mtsinje utasefukira, madzi anawomba nyumbayo, koma sanathe kuigwedeza chifukwa anaimanga bwino.+