Luka 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kumeneko kapolo wa mtsogoleri wina wa asilikali, amene mtsogoleriyo ankamukonda kwambiri, ankadwala ndipo anali atatsala pangʼono kumwalira.+
2 Kumeneko kapolo wa mtsogoleri wina wa asilikali, amene mtsogoleriyo ankamukonda kwambiri, ankadwala ndipo anali atatsala pangʼono kumwalira.+