Luka 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yesu atamva zimenezi anadabwa ndi munthu ameneyu. Kenako anatembenukira gulu la anthu omwe ankamutsatira nʼkuwauza kuti: “Kunena zoona, ngakhale mu Isiraeli sindinapezemo aliyense wachikhulupiriro chachikulu ngati chimenechi.”+
9 Yesu atamva zimenezi anadabwa ndi munthu ameneyu. Kenako anatembenukira gulu la anthu omwe ankamutsatira nʼkuwauza kuti: “Kunena zoona, ngakhale mu Isiraeli sindinapezemo aliyense wachikhulupiriro chachikulu ngati chimenechi.”+