Luka 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma anthu amene anatumidwa aja atabwerera kunyumba, anakapeza kapolo uja ali bwinobwino.+