-
Luka 7:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Patangopita kanthawi pangʼono, ananyamuka kupita kumzinda wina wotchedwa Naini. Ophunzira ake ndiponso gulu lalikulu la anthu linkayenda naye limodzi.
-